Genesis 17:10 - Buku Lopatulika10 Ili ndi pangano langa limene uzisunga pakati pa Ine ndi iwe ndi mbeu zako za pambuyo pako: azidulidwa amuna onse a mwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ili ndi pangano langa limene uzisunga pakati pa Ine ndi iwe ndi mbeu zako za pambuyo pako: azidulidwa amuna onse a mwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Iwe pamodzi ndi zidzukulu zako, muyenera kusunga chipangano ichi chakuti mwamuna aliyense pakati panupa aziwumbalidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iwe pamodzi ndi zidzukulu zako zobwera pambuyo pako muzisunga pangano ili loti mwamuna aliyense pakati panupa azichita mdulidwe. Onani mutuwo |