Genesis 16:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo mthenga wa Yehova anampeza iye pa kasupe wa madzi m'chipululu, pa kasupe wa panjira ya ku Suri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo mthenga wa Yehova anampeza iye pa kasupe wa madzi m'chipululu, pa kasupe wa pa njira ya ku Suri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mngelo wa Chauta adakumana naye pa chitsime m'chipululu, pa mseu wopita ku Suri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mngelo wa Yehova anamupeza Hagara pafupi ndi chitsime mʼchipululu. Chinali chitsime chimene chili mʼmphepete mwa msewu wopita ku Suri. Onani mutuwo |