Genesis 15:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anati, Ambuye Mulungu, nanga ndidzadziwa bwanji kuti lidzakhala cholowa changa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anati, Ambuye Mulungu, nanga ndidzadziwa bwanji kuti lidzakhala cholowa changa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Koma Abramu adati, “Ambuye Chauta, kodi ndingadziŵe bwanji kuti dziko limeneli lidzakhaladi langa?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Koma Abramu anati, “Haa! Ambuye Yehova, kodi ndingadziwe bwanji kuti lidzakhaladi langa?” Onani mutuwo |