Genesis 15:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo anakhulupirira Yehova, ndipo kunayesedwa kwa iye chilungamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo anakhulupirira Yehova, ndipo kunayesedwa kwa iye chilungamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Apo Abramu adakhulupirira Chauta, ndipo chifukwa cha chimenecho, Chauta adamuwona kuti ndi wolungama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Abramu anakhulupirira Yehova, ndipo ichi chinamuchititsa kukhala wolungama. Onani mutuwo |