Genesis 15:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo linalinkulowa dzuwa, ndi tulo tatikulu tinamgwera Abramu: ndipo taonani, kuopsa kwa mdima waukulu kunamgwera iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo linalinkulowa dzuwa, ndi tulo tatikulu tinamgwera Abramu: ndipo taonani, kuopsa kwa mdima waukulu kunamgwera iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pamene dzuŵa linkaloŵa, Abramu adagwidwa ndi tulo tofanato, ndiponso adachita mantha kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pamene dzuwa limalowa Abramu anagona tulo tofa nato ndipo mdima wandiweyani ndi wochititsa mantha unamuphimba. Onani mutuwo |