Genesis 14:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo panali masiku a Amurafere mfumu ya Sinara, ndi Ariyoki mfumu ya Elasara, ndi Kedorilaomere mfumu ya Elamu, ndi Tidala mfumu ya Goimu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo panali masiku a Amurafere mfumu ya Sinara, ndi Ariyoki mfumu ya Elasara, ndi Kedorilaomere mfumu ya Elamu, ndi Tidala mfumu ya Goimu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Masiku amenewo, Amurafere mfumu ya ku Sinara, Ariyoki mfumu ya ku Elasara, Kedorilaomere mfumu ya ku Elamu, ndi Tidala mfumu ya ku Goimu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pa nthawi imeneyi Amarafeli mfumu ya Sinara, Arioki mfumu ya Elasara, Kedorilaomere mfumu ya Elamu ndi Tidala mfumu ya Goimu Onani mutuwo |