Genesis 13:17 - Buku Lopatulika17 Tauka, nuyendeyende m'dzikoli m'litali mwake ndi m'mimba mwake; chifukwa kuti ndidzakupatsa iwe limenelo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Tauka, nuyendeyende m'dzikoli m'litali mwake ndi m'mimba mwake; chifukwa kuti ndidzakupatsa iwe limenelo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Nyamuka tsopano, uyendere dziko lonselo, chifukwa ndakupatsa,” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Dzuka ndipo uyendere dziko lonseli mulitali ndi mulifupi pakuti ndalipereka kwa iwe.” Onani mutuwo |