Genesis 12:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Abramu anapitirira m'dzikomo kufikira ku malo a Sekemu, kufikira ku mtengo wathundu wa ku More. Akanani anali m'dzikomo nthawi yomweyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Abramu anapitira m'dziko kufikira ku malo a Sekemu, kufikira ku mtengo wathundu wa ku More. Akanani anali m'dzikomo nthawi yomweyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Abramuyo adayendera dziko lonselo mpaka adakafika ku Sekemu, ku mtengo wa thundu wa ku More. Pa nthaŵi imeneyo nkuti Akanani akadalimo m'dzikomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Abramu anadutsa mʼdzikomo mpaka kukafika ku Sekemu pa mtengo wa thundu wa ku More. Nthawi imeneyo Akanaani analipobe mʼdzikomo. Onani mutuwo |