Genesis 11:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Yehova anabalalitsa iwo padziko lonse lapansi, ndipo analeka kumanga mzinda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Yehova anabalalitsa iwo pa dziko lonse lapansi, ndipo analeka kumanga mudzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Motero Chauta adaŵamwaza anthuwo pa dziko lonse lapansi, ndipo iwowo adaleka kumanga mzindawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Choncho Yehova anabalalitsa anthu aja pa dziko lonse lapansi ndipo analeka kumanga mzindawo. Onani mutuwo |