Genesis 11:7 - Buku Lopatulika7 Tiyeni, titsike, pomwepo tisokoneze chinenedwe chao, kuti wina asamvere chinenedwe cha mnzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Tiyeni, titsike, pomwepo tisokoneze chinenedwe chao, kuti wina asamvere chinenedwe cha mnzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tiyeni titsikire komweko, tikasokoneze chilankhulo chao kuti asamvane.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Tiyeni titsikireko tikasokoneze chiyankhulo chawo kuti asamamvetsetsane.” Onani mutuwo |