Genesis 11:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo panali pamene anayendayenda ulendo kum'mawa, anapeza chigwa m'dziko la Sinara, ndipo anakhala kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo panali pamene anayendayenda ulendo kum'mawa, anapeza chigwa m'dziko la Sinara, ndipo anakhala kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Atasamukira chakuvuma, adakafika ku chigwa ku dziko la Sinara kumene adakhazikika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pamene anthu amapita chakummawa anapeza chigwa ku dziko la Sinara nakhazikikako. Onani mutuwo |