Genesis 10:21 - Buku Lopatulika21 Ndiponso kwa Semu atate wa ana onse a Eberi, mkulu wa Yafeti, kwa iye kunabadwa ana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndiponso kwa Semu atate wa ana onse a Eberi, mkulu wa Yafeti, kwa iye kunabadwa ana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Semu ndiye kholo la ana onse a Eberi, ndiponso ndiye mkulu wake wa Yafeti. Iyeyu anali ndi ana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Semu amene anali mkulu wake wa Yafeti nayenso anabereka nakhala kholo la Eberi. Onani mutuwo |