Genesis 10:20 - Buku Lopatulika20 Amenewa ndi ana aamuna a Hamu monga mwa mabanja ao, mwa zinenedwe zao, m'maiko ao, m'mitundu yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Amenewa ndi ana amuna a Hamu monga mwa mabanja ao, mwa zinenedwe zao, m'maiko ao, m'mitundu yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ameneŵa ndiwo ana a Hamu ndipo ankakhala m'mafuko osiyanasiyana, ndi m'maiko osiyanasiyana. Fuko lililonse linkalankhula chilankhulo chakechake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Amenewa ndiwo ana aamuna a Hamu monga mwa mafuko ndi ziyankhulo zawo, mʼmadera omwe amakhala ndi mitundu yawo. Onani mutuwo |