Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 1:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachisanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachisanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Tsono kudali madzulo ndiponso m'maŵa, tsiku lachisanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku lachisanu.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 1:23
6 Mawu Ofanana  

Mulungu ndipo anadalitsa zimenezo, nati, Zibalane, zichuluke, zidzaze madzi a m'nyanja, ndi mbalame zichuluke padziko lapansi.


Ndipo adati Mulungu, Dziko lapansi libale zamoyo monga mwa mitundu yao, ng'ombe, ndi zokwawa, ndi zinyama za dziko lapansi monga mwa mitundu yao: ndipo kunatero.


Ndipo anaziona Mulungu zonse zimene adazipanga, ndipo, taonani, zinali zabwino ndithu. Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachisanu ndi chimodzi.


Ndipo Mulungu anatcha kuyerako Usana, ndi mdimawo anautcha Usiku. Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku loyamba.


Ndipo Mulungu analitcha thambolo Kumwamba. Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachiwiri.


Ndipo Yesu ananena naye, Ndithu ndinena ndi iwe, kuti lero, usiku uno, tambala asanalire kawiri, udzandikana Ine katatu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa