Eksodo 9:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo lidzakhala fumbi losalala padziko lonse la Ejipito, ndipo lidzakhala pa anthu ndi pa zoweta ngati zilonda zobuka ndi matuza, m'dziko lonse la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo lidzakhala fumbi losalala pa dziko lonse la Ejipito, ndipo lidzakhala pa anthu ndi pa zoweta ngati zilonda zobuka ndi matuza, m'dziko lonse la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Phulusalo lidzaulukira m'dziko lonse la Ejipito ngati fumbi. Ndipo konse kumene lidzaulukireko, kudzabuka zithupsa zomaphulika ndi kusanduka zilonda pa anthu ndi pa nyama zomwe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Phulusalo lidzasanduka fumbi pa dziko lonse la Igupto. Tsono fumbilo lidzasanduka zithupsa zomaphulika nʼkukhala zilonda pa munthu aliyense ndi pa nyama zomwe mʼdziko lonse la Igupto.” Onani mutuwo |