Eksodo 9:35 - Buku Lopatulika35 Potero mtima wa Farao unalimba, ndipo sanalole ana a Israele amuke; monga Yehova adalankhula mwa Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Potero mtima wa Farao unalimba, ndipo sanalole ana a Israele amuke; monga Yehova adalankhula mwa Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Adakhala wokanika kwambiri, ndipo sadalole kuti Aisraele apite monga momwe Chauta adaauzira Mose muja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Choncho Farao sanalole kuti Aisraeli apite monga momwe Yehova anamuwuzira Mose. Onani mutuwo |