Eksodo 9:34 - Buku Lopatulika34 Pamene Farao anaona kuti mvula ndi matalala ndi mabingu zidaleka anaonjezanso kuchimwa, naumitsa mtima wake, iye ndi anyamata ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Pamene Farao anaona kuti mvula ndi matalala ndi mabingu zidaleka anaonjezanso kuchimwa, naumitsa mtima wake, iye ndi anyamata ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Farao ataona kuti mvula, matalala ndi mabingu, zonsezo zaleka, adakhala wokanikabe, nauma ndithu mtima iyeyo ndi nduna zake zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Farao ataona kuti mvula, matalala ndi mabingu zaleka, anachimwanso. Iye ndi nduna zake anawumitsanso mitima yawo. Onani mutuwo |