Eksodo 8:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo achule adzakwera pa iwe, ndi pa anthu ako, ndi pa anyamata ako onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo achule adzakwera pa iwe, ndi pa anthu ako, ndi pa anyamata ako onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Azidzakulumphira iwe, pamodzi ndi anthu ako, ndi nduna zako zonse.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Achulewo adzakulumphira iwe ndi anthu ako ndiponso nduna zako.” Onani mutuwo |