Eksodo 8:25 - Buku Lopatulika25 Pamenepo Farao anaitana Mose ndi Aroni, nati, Mukani, mphereni nsembe Mulungu wanu m'dzikomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pamenepo Farao anaitana Mose ndi Aroni, nati, Mukani, mphereni nsembe Mulungu wanu m'dzikomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono Farao adaitana Mose ndi Aroni naŵauza kuti, “Pitani mukapereke nsembe kwa Mulungu wanu m'dziko mommuno.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Kenaka Farao anayitanitsa Mose ndi Aaroni nati, “Pitani kaperekeni nsembe kwa Mulungu wanu mʼdziko lomwe lino.” Onani mutuwo |