Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 5:5 - Buku Lopatulika

5 Farao anatinso, Taonani, anthu a m'dziko ndiwo ambiri tsopano; ndipo inu muwapumitsa ku akatundu ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Farao anatinso, Taonani, anthu a m'dziko ndiwo ambiri tsopano; ndipo inu muwapumitsa ku akatundu ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Farao adapitirira kuŵauza kuti, “Anthu ameneŵa akuchulukana kwambiri tsopano. Bwanji inu mufuna kuŵaletsa kugwira ntchito yao?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ndiponso Farao anati, “Taonani, anthuwa mʼdziko muno alipo ochuluka, ndipo inu mukuwaletsa kugwira ntchito.”

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 5:5
5 Mawu Ofanana  

nalankhula nao monga mwa uphungu wa achinyamata, nati, Atate wanga analemeretsa goli lanu, koma ine ndidzaonjezerapo pa goli lanu; atate wanga anakukwapulani ndi zikoti, koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira.


Ndipo tsopano, popeza atate wanga anakusenzetsani goli lolemera, ine ndidzaonjezerapo pa goli lanu; atate wanga anakukwapulani ndi zikoti, koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira.


Ndipo kunali masiku amenewo, atakula Mose, kuti anatulukira kukazonda abale ake, napenya akatundu ao; ndipo anaona munthu Mwejipito ali kukantha Muhebri, wa abale ake.


Mu unyinji wa anthu muli ulemu wa mfumu; koma popanda anthu kalonga aonongeka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa