Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 5:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ndiponso Farao anati, “Taonani, anthuwa mʼdziko muno alipo ochuluka, ndipo inu mukuwaletsa kugwira ntchito.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Farao anatinso, Taonani, anthu a m'dziko ndiwo ambiri tsopano; ndipo inu muwapumitsa ku akatundu ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Farao anatinso, Taonani, anthu a m'dziko ndiwo ambiri tsopano; ndipo inu muwapumitsa ku akatundu ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Farao adapitirira kuŵauza kuti, “Anthu ameneŵa akuchulukana kwambiri tsopano. Bwanji inu mufuna kuŵaletsa kugwira ntchito yao?”

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 5:5
5 Mawu Ofanana  

Anatsatira malangizo amene anyamata anzake anamupatsa ndipo anati “Abambo anga ankakusenzetsani goli lolemetsa. Ine ndidzachititsa kuti likhale lolemera kwambiri. Abambo anga ankakukwapulani ndi zikoti wamba koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira.”


Abambo anga anakusenzetsani goli lolemetsa koma ine ndidzalichititsa kukhala lolemetsa kwambiri. Abambo anga anakukwapulani ndi zikoti wamba koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira.’ ”


Tsiku lina, Mose atakula, anapita kumene kunali anthu a mtundu wake ndipo anawaona akugwira ntchito yowawa. Iye anaona Mwigupto akumenya Mhebri, mmodzi mwa anthu a mtundu wake.


Gulu lalikulu la anthu ndiye ulemerero wa mfumu, koma popanda anthu kalonga amawonongeka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa