Eksodo 39:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo anapanga miliu ya golide woona, napakiza miliu ndi makangaza, pa mkawo wa mwinjiro pozungulira, popakiza ndi makangaza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo anapanga miliu ya golide woona, napakiza miliu ndi makangaza, pa mkawo wa mwinjiro pozungulira, popakiza ndi makangaza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Adapanganso timabelu ta golide wabwino kwambiri, mopakiza pakati pa makangazawo, kuzungulira mpendero wonse wam'munsiwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ndipo anapanga maberu agolide wabwino kwambiri ndipo analumikiza mozungulira mpendero pakati pa makangadzawo. Onani mutuwo |