Eksodo 39:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo anaomba mwinjiro wa efodi, ntchito yoomba ya lamadzi lokha; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo anaomba mwinjiro wa efodi, ntchito yoomba ya lamadzi lokha; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Adapanga mkanjo wake wa efodi, woombedwa ndi nsalu yobiriŵira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Anayipangira efodiyo mkanjo wamtundu wa mtambo, wolukidwa ndi mmisiri waluso. Onani mutuwo |