Eksodo 37:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo pa choikaponyali chomwe panali zikho zinai zopangika ngati katungurume, mitu yake ndi maluwa ake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo pa choikapo nyali chomwe panali zikho zinai zopangika ngati katungurume, mitu yake ndi maluwa ake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pa thunthu lake la choikaponyalecho panali zikho zinai zonga maluŵa amtowo okhala ndi nkhunje zake ndi maluŵa ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Pa choyikapo nyalecho panali zikho zinayi zokhala ngati maluwa amtowo, mphukira ndi maluwa ake. Onani mutuwo |