Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 35:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo Mose ananena ndi khamu lonse la ana a Israele, ndi kuti, Ichi ndi chimene Yehova analamula ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo Mose ananena ndi khamu lonse la ana a Israele, ndi kuti, Ichi ndi chimene Yehova anauza ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Mose adauza Aisraele onse aja kuti, “Chauta akukulamulani kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Mose ananena kwa gulu lonse la Aisraeli kuti, “Zimene Yehova wakulamulirani ndi izi:

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 35:4
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Ine, taona, ndampatsa Oholiyabu, mwana wa Ahisamaki, wa fuko la Dani, akhale naye; ndipo ndaika luso m'mitima ya onse a mtima waluso, kuti apange zonse ndakuuza iwe;


Musamasonkha moto m'nyumba zanu zilizonse tsiku la Sabata.


Mumtengere Yehova chopereka cha mwa zanu; aliyense wa mtima womfunitsa mwini abwere nacho, ndicho chopereka cha Yehova; golide, ndi siliva, ndi mkuwa;


Potero anatsiriza ntchito yonse ya Kachisi wa chihema chokomanako; ndipo ana a Israele adachita monga mwa zonse Yehova adamuuza Mose, anachita momwemo.


Ndipo ukaikemo likasa la mboni, nutchinge likasalo ndi nsalu yotchingayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa