Eksodo 34:3 - Buku Lopatulika3 Palibe munthu akwere ndi iwe, asaonekenso munthu aliyense m'phiri monse; ndi zoweta zazing'ono kapena zoweta zazikulu zisadye kuphiri kuno. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Palibe munthu akwere ndi iwe, asaonekenso munthu aliyense m'phiri monse; ndi zoweta zazing'ono kapena zoweta zazikulu zisadye kuphiri kuno. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Usabwere ndi wina aliyense, ndipo wina asaoneke pa mbali iliyonse ya phirilo. Nkhosa kapena ng'ombe zisadzadye pa tsinde la phirilo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Palibe amene abwere nawe kapena kuoneka pena paliponse pafupi ndi phiri. Ndipo ngakhale nkhosa kapena ngʼombe zisadye mʼmbali mwa phirilo.” Onani mutuwo |