Eksodo 34:26 - Buku Lopatulika26 Uzibwera nazo zipatso zoyambayamba za nthaka yako kunyumba ya Yehova Mulungu wako. Usaphika mwanawambuzi mu mkaka wa make. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Uzibwera nazo zipatso zoyambayamba za nthaka yako kunyumba ya Yehova Mulungu wako. Usaphika mwanawambuzi mu mkaka wa make. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Muzibwera ndi zokolola zoyamba ndi zabwino kwambiri ku Nyumba ya Chauta, Mulungu wanu. Musaphike kamwanakanyama mu mkaka wa make.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 “Muzibwera ndi zipatso zoyambirira kucha zabwino kwambiri ku nyumba ya Yehova Mulungu wanu. “Musamaphike kamwana kambuzi mu mkaka wa mayi wake.” Onani mutuwo |