Eksodo 34:23 - Buku Lopatulika23 Amuna ako onse azioneka pamaso pa Yehova Mulungu, Mulungu wa Israele, katatu chaka chimodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Amuna ako onse azioneka pamaso pa Yehova Mulungu, Mulungu wa Israele, katatu chaka chimodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Amuna onse azibwera pamaso pa Ine Chauta, Mulungu wa Aisraele, katatu pa chaka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Amuna onse azionekera pamaso pa Yehova Mulungu wa Israeli, katatu pa chaka. Onani mutuwo |
Koma pofika anthu a m'dziko pamaso pa Yehova m'zikondwerero zoikika, iye amene alowera njira ya kuchipata cha kumpoto kudzalambira, atulukire njira ya kuchipata cha kumwera; ndi iye amene alowera njira ya kuchipata cha kumwera, atulukire njira ya kuchipata cha kumpoto; asabwerere njira ya chipata anadzeracho, koma atulukire m'tsogolo mwake.