Eksodo 33:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Yehova anati, Taona pali Inepo pali malo, ndipo uime pathanthwe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Yehova anati, Taona pali Inepo pali malo, ndipo uime pathanthwe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Adapitirira kunenanso kuti, “Pafupi ndi Ine pano pali thanthwe, iwe uimirire pathanthwepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ndipo Yehova anati, “Pali malo pafupi ndi ine pomwe ungathe kuyima pa thanthwe. Onani mutuwo |