Eksodo 33:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo ananena ndi Iye, Ikapanda kumuka nane nkhope yanu, musatikweze kuchokera kuno. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo ananena ndi Iye, Ikapanda kumuka nane nkhope yanu, musatikweze kuchokera kuno. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Apo Mose adauza Chauta kuti, “Mukapanda kupita nafe limodzi, musatilole kuti tichoke pano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kenaka Mose anati kwa Yehova, “Ngati inu simupita nafe, musatitumize kuti tipite, kutichotsa pano. Onani mutuwo |