Eksodo 32:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Ndawapenya anthu awa, taona, ndiwo anthu opulupudza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Ndawapenya anthu awa, taona, ndiwo anthu opulupudza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndipo Chauta adaonjeza kuti, “Anthu ameneŵa ndikuŵadziŵa, ngokanika kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yehova anati kwa Mose, “Ine ndikuwadziwa anthu amenewa. Iwowa ndi ankhutukumve. Onani mutuwo |