Eksodo 32:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo Yehova anakantha anthu, chifukwa anapanga mwanawang'ombe amene Aroni anapanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo Yehova anakantha anthu, chifukwa anapanga mwanawang'ombe amene Aroni anapanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Motero Chauta adatumiza nthenda pa anthuwo, chifukwa choti adakakamiza Aroni kuti aŵapangire fano la mwanawang'ombe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Ndipo Yehova anawakantha anthuwo ndi mliri chifukwa anawumiriza Aaroni kuti awapangire fano la mwana wangʼombe. Onani mutuwo |