Eksodo 32:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo pamene Mose anaona kuti anthu anamasuka, popeza Aroni adawamasula kuti awatonze adani ao, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo pamene Mose anaona kuti anthu anamasuka, popeza Aroni adawamasula kuti awatonze adani ao, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Mose adaonadi kuti anthuwo ngosokonezeka, (chifukwa Aroni adaaŵalekerera, mpaka iwo kusanduka anthu oŵanyodola pakati pa adani ao). Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Mose anaona kuti anthuwo anali osokonezekadi chifukwa Aaroni anawalekerera mpaka kusanduka anthu osekedwa pakati pa adani awo. Onani mutuwo |