Eksodo 32:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Yehova analeka choipa adanenachi, kuwachitira anthu ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Yehova analeka choipa adanenachi, kuwachitira anthu ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Choncho Chauta adaleka chilango choopsa chimene adaati agwetsere anthu akewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Choncho Yehova analeka ndipo sanawachitire choyipa anthu ake monga anaopsezera. Onani mutuwo |