Eksodo 30:38 - Buku Lopatulika38 Aliyense wokonza china chotere kununkhizapo, achotsedwe kwa anthu a mtundu wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Aliyense wokonza china chotere kununkhizapo, asadzidwe kwa anthu a mtundu wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Ngati munthu wina apanga lubani wofanafana ndi ameneyu kuti amve fungo lake lokoma, azichotsedwa pakati pa anthu anzake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Aliyense amene adzapanga wofanana naye kuti asangalale ndi fungo lake ayenera kuchotsedwa pakati pa anthu anzake.” Onani mutuwo |