Eksodo 30:37 - Buku Lopatulika37 Koma za chofukizacho uchikonze, musadzikonzere nokha china, mwa makonzedwe ake amene; muchiyese chopatulika cha Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Koma za chofukizacho uchikonze, musadzikonzere nokha china, mwa makonzedwe ake amene; muchiyese chopatulika cha Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Ndipo lubani amene upangeyo potsata mapangidwe ake, asadzakhalire inuyo ai, koma adzakhale woyera wokhalira Chauta yekha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Musapange lubani wanu potsatira njira iyi. Lubani yense wopangidwa mwa njira iyi akhale wopatulika, woperekedwa kwa Yehova. Onani mutuwo |