Eksodo 30:35 - Buku Lopatulika35 ndipo uzikonza nazo chofukiza, chosakaniza mwa machitidwe a wosakaniza, chokometsera ndi mchere, choona, chopatulika; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 ndipo uzikonza nazo chofukiza, chosanganiza mwa machitidwe a wosanganiza, chokometsera ndi mchere, choona, chopatulika; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Uphatikize pamodzi zonsezi, ndipo upange lubani monga amachitira mmisiri wopanga zonunkhira. Athiremo mchere, ndipo akhale woyera ndi wopatulika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Uziphatikize pamodzi zonsezi ndi kupanga lubani monga amachitira mmisiri wopanga zonunkhira. Athire mchere ndipo akhale woyera ndi wopatulika. Onani mutuwo |