Eksodo 30:31 - Buku Lopatulika31 Nulankhule ndi ana a Israele, ndi kuti, Awa ndi mafuta odzoza opatulika a Ine mwa mibadwo yanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Nulankhule ndi ana a Israele, ndi kuti, Awa ndi mafuta odzoza opatulika a Ine mwa mibadwo yanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Tsono Aisraele onse udzaŵauze kuti, ‘Ameneŵa ndiwo adzakhale mafuta anga oyera odzozera pa mibadwo yanu yonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Tsono awuze a Israeli kuti, mafuta wodzozera awa adzakhala wopatulika mpaka muyaya. Onani mutuwo |