Eksodo 30:28 - Buku Lopatulika28 ndi guwa la nsembe lofukizapo, ndi guwa la nsembe yopsereza ndi zipangizo zake zonse, ndi mkhate wosambiramo ndi tsinde lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 ndi guwa la nsembe lofukizapo, ndi guwa la nsembe yopsereza ndi zipangizo zake zonse, ndi mkhate wosambiramo ndi tsinde lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 guwa lopserezapo zopereka, pamodzi ndi zipangizo zake, ndiponso beseni losambiramo lija ndi phaka lake lomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 guwa lansembe yopsereza ndi ziwiya zake zonse, ndiponso beseni pamodzi ndi nsichi yake. Onani mutuwo |