Eksodo 30:27 - Buku Lopatulika27 ndi guwalo ndi zipangizo zake zonse, ndi choikaponyali ndi zipangizo zake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 ndi gomelo ndi zipangizo zake zonse, ndi choikapo nyali ndi zipangizo zake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 tebulo ndi zipangizo zake zonse, choikaponyale pamodzi ndi zida zake, guwa lofukizirapo lubani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 tebulo, ndi ziwiya zake zonse, choyikapo nyale ndi zipangizo zake, guwa lofukizirapo lubani, Onani mutuwo |