Eksodo 30:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo Aroni ndi ana ake aamuna azisambiramo manja ao ndi mapazi ao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo Aroni ndi ana ake amuna azisambiramo manja ao ndi mapazi ao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Aroni ndi ana ake azisamba m'manja ndi kutsuka mapazi ao ndi madzi amenewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Aaroni ndi ana ake azisamba mʼmanja ndi kutsuka mapazi awo ndi madzi amenewo. Onani mutuwo |