Eksodo 3:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Mose anati kwa Mulungu, Onani, pakufika ine kwa ana a Israele, ndi kunena nao, Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu; ndipo akakanena ndi ine, Dzina lake ndani? Ndikanena nao chiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Mose anati kwa Mulungu, Onani, pakufika ine kwa ana a Israele, ndi kunena nao, Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu; ndipo akakanena ndi ine, Dzina lake ndani? Ndikanena nao chiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mose adayankha kuti, “Tsono ine ndikapita kwa Aisraelewo kukaŵauza kuti Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu, iwowo akakandifunsa kuti, ‘Dzina lake ndani?’ Ndiye ineyo ndikaŵauze chiyani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mose anati kwa Mulungu, “Ngati ndipita kwa Aisraeli ndi kukawawuza kuti, ‘Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu,’ ndipo iwo nʼkukandifunsa kuti ‘Dzina lake ndi ndani?’ Tsono ine ndikawawuze chiyani?” Onani mutuwo |