Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 29:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo ubwere nao ana ake aamuna ndi kuwaveka malaya am'kati.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo ubwere nao ana ake amuna ndi kuwaveka malaya am'kati.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Kenaka ubwere ndi ana ake aamuna, ndipo uŵaveke miinjiro.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ubwere ndi ana ake aamuna ndipo uwavekenso minjiro

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 29:8
4 Mawu Ofanana  

Ndipo upikule malaya am'kati abafuta a thonje losansitsa, nusoke nduwira wabafuta, nusokenso mpango wopikapika.


Ndipo usokere ana a Aroni malaya am'kati, nuwasokere mipango; uwasokerenso akapa akhale aulemerero ndi okoma.


Ndipo ubwere nao ana ake aamuna ndi kuwaveka malaya am'kati;


Ndipo Mose anatenga ana a Aroni, nawaveka malaya a m'kati, nawamanga m'chuuno ndi mipango, nawamanga akapa; monga Yehova adzauza Mose.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa