Eksodo 29:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo utenge nkhosa yamphongo yodzaza manja, nuphike nyama yake m'malo opatulika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo utenge nkhosa yamphongo yodzaza manja, nuphike nyama yake m'malo opatulika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 “Tsono utenge nkhosa yamphongo yophera mwambo woloŵera unsembe, uiphike m'malo oyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 “Utenge nkhosa yayimuna ya pamwambo wodzoza ansembe ndipo uyiphike pamalo opatulika. Onani mutuwo |
Pamenepo anati kwa ine, Zipinda za kumpoto, ndi zipinda za kumwera, zili chakuno cha mpatawo, ndizo zipinda zopatulika, kumene ansembe okhala pafupi pa Yehova azidyera zinthu zopatulika kwambiri; kumeneko aziika zopatulika kwambiri, ndi nsembe yaufa, ndi nsembe yauchimo, ndi nsembe yopalamula; pakuti malowo ndi opatulika.