Eksodo 29:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo uziike mu dengu limodzi, ndi kubwera nazo mudengu, pamodzi ndi ng'ombe yamphongo ndi nkhosa ziwiri zamphongo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo uziike mu dengu limodzi, ndi kubwera nazo mudengu, pamodzi ndi ng'ombe yamphongo ndi nkhosa ziwiri zamphongo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Uziike m'lichero, ndipo ubwere nazo kwa Ine, pamene ukupereka nsembe ng'ombe yamphongo ija ndi nkhosa zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Uziyike mʼdengu ndipo ubwere nazo kwa Ine pamodzi ndi ngʼombe yayimuna ija ndi nkhosa ziwiri zazimuna zija. Onani mutuwo |