Eksodo 29:16 - Buku Lopatulika16 Nuiphe nkhosa yamphongoyo, ndi kutenga mwazi wake, ndi kuuwaza paguwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Nuiphe nkhosa yamphongoyo, ndi kutenga mwazi wake, ndi kuuwaza pa guwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono uiphe ndipo utenge magazi ake ndi kuwaza pa mbali zonse za guwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Uyiphe ndipo utenge magazi ake ndi kuwaza mbali zonse zaguwalo. Onani mutuwo |