Eksodo 28:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo uombe mwinjiro wa efodi ndi lamadzi lokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo uombe mwinjiro wa efodi ndi lamadzi lokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 “Upange mkanjo wa nsalu yobiriŵira, wophimba chovala cha efodi chija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 “Uyipangire efodiyo mkanjo wamtundu wa mtambo. Onani mutuwo |