Eksodo 28:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo amange chapachifuwa pa mphete zake ndi mphete za efodi ndi mkuzi wamadzi, kuti chikhale pa mpango wa efodi; ndi kuti chapachifuwa chisamasuke paefodi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo amange chapachifuwa pa mphete zake ndi mphete za efodi ndi mkuzi wamadzi, kuti chikhale pa mpango wa efodi; ndi kuti chapachifuwa chisamasuke paefodi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Tsono ulumikize mphete za chovala chapachifuwacho ku mphete za chovala cha efodi chija ndi kamkuzi kobiriŵira, kuti chovala chapachifuwacho chikhale pamwamba pa lamba wolukidwa mwaluso uja, ndipo chovala chapachifuwa chilumikizike bwino ku chovala cha efodi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Tsono umangirire mphete za pa chovala chapachifuwa zija ku mphete za efodi ndi chingwe chamtundu wa mtambo, kulumikiza lamba ndi chovala chapachifuwacho kuti chovala chapachifuwacho chisalekane ndi efodi. Onani mutuwo |