Eksodo 28:27 - Buku Lopatulika27 Upangenso mphete ziwiri zagolide, ndi kuzimanga pa zapamapewa ziwiri za efodi, m'munsi, ku mbali yake ya kutsogolo, pafupi pa msoko wake, pamwamba pa mpango wa efodi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Upangenso mphete ziwiri zagolide, ndi kuzimanga pa zapamapewa ziwiri za efodi, m'munsi, ku mbali yake ya kutsogolo, pafupi pa msoko wake, pamwamba pa mpango wa efodi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Upangenso mphete zina ziŵiri zagolide, ndipo uzilumikize cham'munsi, kutsogolo kwake kwa malamba aŵiri a pa mapewa a efodi, pafupi ndi misoko, pa lamba wolukidwa mwaluso uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Upangenso mphete zina ziwiri zagolide ndipo uzilumikize kumunsi kwa tinsalu takutsogolo kwa efodi, pafupi ndi msoko, pamwamba pangʼono pa lamba wamʼchiwuno wa efodi. Onani mutuwo |