Eksodo 28:25 - Buku Lopatulika25 Koma nsonga zake ziwiri za maunyolo opotawo uzimange ku zoikamo ziwiri, ndi kuziika pa zapamapewa ziwiri za efodi, m'tsogolo mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Koma nsonga zake ziwiri za maunyolo opotawo uzimange ku zoikamo ziwiri, ndi kuziika pa zapamapewa ziwiri za efodi, m'tsogolo mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Ndipo nsonga zake zina ziŵiri za zingwezo uzimange ku zoikamo zake zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ndipo mbali ina ya timaunyoloto umangirire pa zoyikapo zake ziwiri zija ndi kulumikiza pa tinsalu takutsogolo kwa mapewa a efodi. Onani mutuwo |